Deuteronomo 28:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+ Yesaya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye waikira chizindikiro mtundu waukulu wakutali.+ Wauimbira likhweru kumapeto kwa dziko lapansi.+ Ndipotu mtunduwo udzachita changu n’kubwera msangamsanga.+
49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+
26 Iye waikira chizindikiro mtundu waukulu wakutali.+ Wauimbira likhweru kumapeto kwa dziko lapansi.+ Ndipotu mtunduwo udzachita changu n’kubwera msangamsanga.+