Yobu 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chiyani mukubisa nkhope yanu,+N’kunditenga ine ngati mdani wanu?+ Yobu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+ Yobu 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mkwiyo wake nawonso wandiyakira,+Ndipo akungondiona ngati ndine mdani wake.
9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+