Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.* Yobu 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndine woyera, wopanda tchimo,+Ndilibe chondidetsa, ndilibe cholakwa.+
14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*