Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+

  • Salimo 132:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ansembe anu avale chilungamo,+

      Ndipo okhulupirika anu afuule mosangalala.+

  • Yesaya 61:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndithu ine ndidzakondwera mwa Yehova.+ Moyo wanga udzasangalala ndi Mulungu wanga.+ Pakuti iye wandiveka zovala zachipulumutso.+ Wandiveka malaya akunja achilungamo odula manja,+ ngati mkwati amene wavala chovala chakumutu mofanana ndi wansembe,+ ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.+

  • Aefeso 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero khalani olimba, mutamanga kwambiri choonadi+ m’chiuno mwanu,+ mutavalanso chodzitetezera pachifuwa chachilungamo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena