Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 29:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+

      Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*

  • Yesaya 61:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndithu ine ndidzakondwera mwa Yehova.+ Moyo wanga udzasangalala ndi Mulungu wanga.+ Pakuti iye wandiveka zovala zachipulumutso.+ Wandiveka malaya akunja achilungamo odula manja,+ ngati mkwati amene wavala chovala chakumutu mofanana ndi wansembe,+ ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.+

  • Zekariya 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo ndinanena kuti: “Auzeni kuti amuveke nduwira* yoyera kumutu kwake.”+ Ndipo anamuvekadi nduwira yoyera kumutu kwake. Anamuvekanso zovala. Apa n’kuti mngelo wa Yehova ataimirira pambali pake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena