Ekisodo 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno umuveke nduwira pamutu pake ndipo panduwirapo uikepo chizindikiro chopatulika cha kudzipereka.+ Levitiko 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
6 Ndiyeno umuveke nduwira pamutu pake ndipo panduwirapo uikepo chizindikiro chopatulika cha kudzipereka.+
9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.