Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Izi zili choncho, mmodzi mwa anyamata a Nabala anauza Abigayeli, mkazi wa Nabala kuti: “Davide anatumiza nthumwi zake kuchokera m’chipululu kudzafunira zabwino mbuyanga, koma mbuyanga walalatira+ nthumwizo.

  • Ezekieli 33:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 akabweza chinthu chimene anatenga kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ akabweza zinthu zimene analanda mwauchifwamba,+ n’kuyamba kuyenda motsatira malamulo opatsa moyo mwa kupewa kuchita zinthu zopanda chilungamo,+ munthuyo adzakhalabe ndi moyo,+ sadzafa ayi.

  • 2 Akorinto 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chifukwa cha umboni umene utumikiwu ukupereka, iwo akulemekeza Mulungu. Akutero chifukwa inuyo mwagonjera uthenga wabwino wonena za Khristu,+ monga mmene mukulengezera poyera, ndiponso chifukwa chakuti mwapereka chopereka kwa iwowo ndi kwa onse mowolowa manja.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena