Ezekieli 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Munthu woipa akasiya zinthu zoipa zimene anali kuchita n’kumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ iyeyu adzapulumutsa moyo wake.+
27 “‘Munthu woipa akasiya zinthu zoipa zimene anali kuchita n’kumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ iyeyu adzapulumutsa moyo wake.+