Ekisodo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Mnzako ukamulanda chovala chake monga chikole,+ uzim’bwezera dzuwa likamalowa. Ezekieli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ngati sazunza munthu aliyense,+ ngati amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ ngati salanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati amapatsa munthu wanjala chakudya+ ndi kuphimba munthu wamaliseche ndi chovala,+
7 ngati sazunza munthu aliyense,+ ngati amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ ngati salanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati amapatsa munthu wanjala chakudya+ ndi kuphimba munthu wamaliseche ndi chovala,+