Deuteronomo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Munthu asalande mnzake mphero kapena mwala woperera monga chikole.+ Kumulanda zimenezi monga chikole ndiko kumulanda moyo. Yobu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Oipa amalanda mwana wamasiye kum’chotsa pabere.+Amatenga ngati chikole chovala chimene wozunzika wavala.+ Amosi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+
6 “Munthu asalande mnzake mphero kapena mwala woperera monga chikole.+ Kumulanda zimenezi monga chikole ndiko kumulanda moyo.
9 Oipa amalanda mwana wamasiye kum’chotsa pabere.+Amatenga ngati chikole chovala chimene wozunzika wavala.+
8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+