Ekisodo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Mnzako ukamulanda chovala chake monga chikole,+ uzim’bwezera dzuwa likamalowa. Deuteronomo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+ Ezekieli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ngati amazunza munthu wosautsika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati sabweza chikole,+ ngati amakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa,+ ndiye kuti wachita chinthu chonyansa.+
13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+
12 ngati amazunza munthu wosautsika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati sabweza chikole,+ ngati amakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa,+ ndiye kuti wachita chinthu chonyansa.+