Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo tikatsatira malamulo onsewa monga mmene Yehova Mulungu wathu watilamulira,+ ndiye kuti tikuchita chilungamo+ pamaso pake.’

  • Salimo 112:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu aumphawi.+

      צ [Tsa·dhehʹ]

      Chilungamo chake chidzakhalapo kwamuyaya.+

      ק [Qohph]

      Nyanga* yake idzakwezedwa ndi ulemerero.+

  • Danieli 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chotero inu mfumu, chonde mverani malangizo anga+ ndipo chotsani machimo anu pochita zolungama.+ Muchotsenso zolakwa zanu pochitira chifundo osauka.+ Mukatero, mwina zinthu zidzapitiriza kukuyenderani bwino kwa nthawi yaitali.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena