1 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+ Salimo 75:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+ Salimo 92:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+
2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+
10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+
10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+