Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+

  • Miyambo 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pali amene amapatsa mowolowa manja, komabe zinthu zake zimawonjezeka.+ Palinso amene safuna kupatsa ena zinthu zoyenera kuwapatsa, koma amangokhala wosowa.+

  • Miyambo 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Wokomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+ ndipo adzam’bwezera zimene anachitazo.+

  • Mlaliki 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pereka gawo la zinthu zimene uli nazo kwa anthu 7, ngakhale 8,+ chifukwa sukudziwa tsoka limene lidzagwe padziko lapansi.+

  • 2 Akorinto 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 (Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Iye wagawira ena mowolowa manja. Wapereka kwa anthu aumphawi, ndipo chilungamo chake chidzakhalapo kwamuyaya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena