Salimo 112:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu osauka.+ צ [Tsade] Chilungamo chake chidzakhalapo mpaka kalekale.+ ק [Qoph] Mphamvu zake zidzawonjezeka* chifukwa cha ulemerero. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 112:9 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, ptsa. 27-28
9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu osauka.+ צ [Tsade] Chilungamo chake chidzakhalapo mpaka kalekale.+ ק [Qoph] Mphamvu zake zidzawonjezeka* chifukwa cha ulemerero.