Deuteronomo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+
10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.