Salimo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+ Salimo 149:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okhulupirika akondwere mu ulemerero.Iwo aimbe mosangalala pamabedi awo.+
11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+