Salimo 133:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 133 Taonani! Ndi zabwino komanso zosangalatsa kwambiriAbale akakhala pamodzi mogwirizana!+