29 Chotero pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene ali m’ndende yapansi, ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+