Yobu 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+
10 Choncho inu amuna a mtima+ womvetsa zinthu, ndimvereni.Mulungu woona sangachite zoipa m’pang’ono pomwe,+Ndipo Wamphamvuyonse sangachite zinthu zopanda chilungamo ngakhale pang’ono.+