Yobu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chonsecho mukudziwa kuti ndine wosalakwa,+Ndipo palibe wondipulumutsa m’manja mwanu.+ Yobu 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chonsecho manja anga sanachite zachiwawa,Ndipo pemphero langa ndi loyera.+ Yobu 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yobu wanena kuti, ‘Ndithu ine si ine wolakwa,+Koma Mulungu wapotoza chiweruzo changa.+