Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika.
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika.