Salimo 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Landitsani moyo wanga ku lupanga,+Moyo wanga wokhawu umene ndili nawo muulanditse m’kamwa mwa galu.+ Salimo 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+
20 Landitsani moyo wanga ku lupanga,+Moyo wanga wokhawu umene ndili nawo muulanditse m’kamwa mwa galu.+ Salimo 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+
4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+