Yobu 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwala kwa oipa kumachotsedwa,+Ndipo dzanja lokwezedwa m’mwamba limathyoledwa.+ Salimo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+
15 Thyolani dzanja la woipa ndi wankhanzayo.+Fufuzani zoipa zake zonse ndi kumulanga kufikira zoipazo zitatha.+