Yobu 34:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kuti munthu wopanduka asalamulire,+Ndi kuti pasakhale misampha+ ya anthu. Yobu 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwala kwa oipa kumachotsedwa,+Ndipo dzanja lokwezedwa m’mwamba limathyoledwa.+ Salimo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti manja a anthu oipa adzathyoledwa,+Koma Yehova adzathandiza anthu olungama.+ Ezekieli 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzathyola dzanja la Farao mfumu ya Iguputo.+ Dzanjalo silidzamangidwa ndi nsalu zomangira pachilonda+ kuti lichire n’kukhalanso lamphamvu kuti lizidzatha kugwira lupanga.” Zekariya 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsoka m’busa wanga wopanda pake+ amene akusiya nkhosa.+ Lupanga lidzamutema padzanja ndi kuboola diso lake la kudzanja lamanja. Dzanja lake lidzafota,+ ndipo diso lake la kudzanja lamanja lidzachita mdima.”
21 “Iwe mwana wa munthu, ine ndidzathyola dzanja la Farao mfumu ya Iguputo.+ Dzanjalo silidzamangidwa ndi nsalu zomangira pachilonda+ kuti lichire n’kukhalanso lamphamvu kuti lizidzatha kugwira lupanga.”
17 Tsoka m’busa wanga wopanda pake+ amene akusiya nkhosa.+ Lupanga lidzamutema padzanja ndi kuboola diso lake la kudzanja lamanja. Dzanja lake lidzafota,+ ndipo diso lake la kudzanja lamanja lidzachita mdima.”