Yobu 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso iye adzakhala chipulumutso changa,+Chifukwa pamaso pake sipadzafika wampatuko.+ Yobu 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi chiyembekezo cha wampatuko n’chiyani Mulungu akachotsa moyo wake,+Akamulanda moyo wake?+