Yobu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndi mmene zilili njira za onse oiwala Mulungu,+Ndipo chiyembekezo cha wampatuko chidzatha.+ Yobu 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi chiyembekezo cha wampatuko n’chiyani Mulungu akachotsa moyo wake,+Akamulanda moyo wake?+ Yobu 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ampatuko adzaunjika mkwiyo.+Iwo sadzalirira thandizo chifukwa chakuti iye wawamanga. Salimo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndani angakwere m’phiri la Yehova?+Ndipo ndani anganyamuke kukalowa m’malo ake opatulika?+ Yesaya 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+
13 Ndi mmene zilili njira za onse oiwala Mulungu,+Ndipo chiyembekezo cha wampatuko chidzatha.+ Yobu 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi chiyembekezo cha wampatuko n’chiyani Mulungu akachotsa moyo wake,+Akamulanda moyo wake?+ Yobu 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ampatuko adzaunjika mkwiyo.+Iwo sadzalirira thandizo chifukwa chakuti iye wawamanga. Salimo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndani angakwere m’phiri la Yehova?+Ndipo ndani anganyamuke kukalowa m’malo ake opatulika?+ Yesaya 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+
14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+