Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ Yesaya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+
2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+