Yobu 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso iye adzakhala chipulumutso changa,+Chifukwa pamaso pake sipadzafika wampatuko.+ Yobu 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ampatuko adzaunjika mkwiyo.+Iwo sadzalirira thandizo chifukwa chakuti iye wawamanga. Aheberi 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+
6 koma tsopano anagwa.+ Anthu amenewa n’zosatheka kuwadzutsanso kuti alape.+ N’zosatheka chifukwa chakuti anthu amenewa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndi kumunyoza poyera.+