Yobu 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga. Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+
7 Yehova atanena mawu amenewa kwa Yobu, Yehovayo anauza Elifazi wa ku Temani kuti:“Mkwiyo wanga wayakira iweyo ndi anzako awiriwo+ chifukwa inu simunanene zoona za ine,+ monga wachitira Yobu mtumiki wanga.