Ekisodo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwapemerera mpweya wanu,+ ndipo nyanja yawamiza.+Amira ngati mtovu m’madzi akuya.+ Machitidwe 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.
23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.