Yobu 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano moyo wanga ukukhuthuka mwa ine.+Masiku a masautso+ ali pa ine. Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]