Yobu 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati ndine wolakwa, tsoka kwa ine!+Ngati ndine wosalakwa, ndisadzutse mutu wanga.+Ndachita manyazi kwambiri ndipo ndadzazidwa ndi mavuto.+
15 Ngati ndine wolakwa, tsoka kwa ine!+Ngati ndine wosalakwa, ndisadzutse mutu wanga.+Ndachita manyazi kwambiri ndipo ndadzazidwa ndi mavuto.+