Salimo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Onani masautso anga ndi mavuto anga,+Ndipo mundichotsere machimo anga onse.+ Salimo 119:153 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 153 Onani kusautsika kwanga ndipo ndipulumutseni,+Pakuti sindinaiwale chilamulo chanu.+