Nyimbo ya Solomo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wachikondi wanga wandiuza kuti, ‘Nyamuka wokondedwa wanga wokongolawe,+ tiye tizipita.+ Chivumbulutso 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Awa ndiwo amene sanadziipitse ndi akazi,+ ndipo ali ngati anamwali.+ Amenewa ndiwo amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ kuchokera mwa anthu, monga zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa.
4 Awa ndiwo amene sanadziipitse ndi akazi,+ ndipo ali ngati anamwali.+ Amenewa ndiwo amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ kuchokera mwa anthu, monga zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa.