1 Mbiri 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya, ndi Eliezere, anali ansembe omwe anali kuimba malipenga mokweza+ patsogolo pa likasa la Mulungu woona. Obedi-edomu ndi Yehiya anali alonda a Likasa.
24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya, ndi Eliezere, anali ansembe omwe anali kuimba malipenga mokweza+ patsogolo pa likasa la Mulungu woona. Obedi-edomu ndi Yehiya anali alonda a Likasa.