1 Akorinto 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chofunika n’chiyani? Ndipemphere ndi mphatso ya mzimu, koma ndipempherenso ndi maganizo anga. Ndiimbe chitamando ndi mphatso ya mzimu,+ koma ndiimbenso ndi maganizo anga.+
15 Ndiye chofunika n’chiyani? Ndipemphere ndi mphatso ya mzimu, koma ndipempherenso ndi maganizo anga. Ndiimbe chitamando ndi mphatso ya mzimu,+ koma ndiimbenso ndi maganizo anga.+