Yeremiya 32:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+ Machitidwe 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iye sanasiyanitse m’pang’ono pomwe pakati pa ife ndi iwo.+ Koma anayeretsa mitima yawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo.+ Aefeso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.
39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+
9 Ndipo iye sanasiyanitse m’pang’ono pomwe pakati pa ife ndi iwo.+ Koma anayeretsa mitima yawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo.+
10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.