Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ndipo anamufunsa kuti: “Kodi ukumva zimene awa akunenazi?” Yesu anayankha kuti: “Inde. Kodi simunawerenge+ zimenezi kuti, ‘M’kamwa mwa ana ndi mwa ana oyamwa mwaikamo mawu otamanda’?”+

  • Luka 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Nthawi yomweyo Yesu anakondwera+ kwambiri mwa mzimu woyera n’kunena kuti: “Atate ndikukutamandani pamaso pa onse, inu Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa zinthu izi mwazibisa kwa anzeru+ ndi ozama m’maphunziro, koma mwaziulula kwa tiana. Inde Atate, chifukwa inu munakonda kuti zinthu zikhale chonchi.

  • Machitidwe 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ataona mmene Petulo ndi Yohane anali kulankhulira molimba mtima, komanso atazindikira kuti anali anthu osaphunzira ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anayamba kuwazindikira kuti anali kuyenda ndi Yesu.+

  • 1 Akorinto 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena