Aheberi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munamutsitsa pang’ono poyerekeza ndi angelo. Munamuveka ulemerero ndi ulemu+ monga chisoti chachifumu, ndipo munamuika kuti alamulire ntchito za manja anu.+
7 Munamutsitsa pang’ono poyerekeza ndi angelo. Munamuveka ulemerero ndi ulemu+ monga chisoti chachifumu, ndipo munamuika kuti alamulire ntchito za manja anu.+