Ezekieli 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Yehova anauza munthu uja kuti: “Uyendeyende mumzinda wonse wa Yerusalemu, ndipo ulembe chizindikiro pamphumi za anthu amene akuusa moyo* ndi kubuula+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene zikuchitika mumzindawu.”+ Zefaniya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+
4 Pamenepo Yehova anauza munthu uja kuti: “Uyendeyende mumzinda wonse wa Yerusalemu, ndipo ulembe chizindikiro pamphumi za anthu amene akuusa moyo* ndi kubuula+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene zikuchitika mumzindawu.”+
3 Akalonga ake anali mikango imene inali kubangula.+ Oweruza ake anali mimbulu yoyenda usiku imene sinatafune mafupa mpaka m’mawa.+