Salimo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemerero wake ndi waukulu m’chipulumutso chanu.+Mwaipatsa ulemu ndi ulemerero.+ Miyambo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti usapereke ulemu wako kwa anthu ena+ kapena kupereka zaka zako ku zinthu zankhanza.+