Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nthawi yomweyo, Davide anauza atumiki ake onse amene anali naye limodzi mu Yerusalemu, kuti: “Nyamukani, tiyeni tithawe,+ pakuti sipapezeka munthu wopulumuka m’manja mwa Abisalomu. Chitani changu, pakuti mwina angafike mofulumira ndi kutipeza n’kutichitira choipa komanso kukantha mzinda ndi lupanga!”+

  • Salimo 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ngati munthu wondichitira zabwino ndamubwezera zoipa,+

      Kapena ngati ndafunkha zinthu za aliyense wondichitira zoipa amene sanaphule kanthu,+

  • Machitidwe 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Nthawi imeneyo m’pamene Mfumu Herode* anayamba kuzunza+ ena a mumpingo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena