Salimo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+ Salimo 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye adzabwezera zoipa kwa adani anga.+Achititseni kukhala chete chifukwa cha choonadi chanu.+ Machitidwe 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode,* Pontiyo Pilato,+ pamodzi ndi anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzinda uno ndi kuukira Yesu, mtumiki wanu woyera,+ amene inu munamudzoza.+
3 Inu Yehova, n’chifukwa chiyani adani anga achuluka chotere?+N’chifukwa chiyani anthu ondiukira achuluka?+
27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode,* Pontiyo Pilato,+ pamodzi ndi anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzinda uno ndi kuukira Yesu, mtumiki wanu woyera,+ amene inu munamudzoza.+