Salimo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+ Salimo 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+
9 Yehova adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo kwa aliyense woponderezedwa,+Adzakhala malo okwezeka ndiponso achitetezo m’nthawi za masautso.+
2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+