Salimo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinaitana inu Yehova,+Ndipo ndinachonderera Yehova kuti andikomere mtima.+ Salimo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lemekezani Yehova pamodzi ndi ine+ anthu inu,Tiyeni tonse tikweze dzina lake.+