Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+ Salimo 77:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Ndidzafuulira Mulungu,+Ndithu, ndidzafuulira Mulungu, ndipo iye adzatchera khutu lake kwa ine.+