2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako. Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+
15 Ndipo kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachoka pa iye monga mmene ndinakuchotsera pa Sauli,+ amene ndinam’chotsa pamaso pako.
13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+