Salimo 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga amandibwezera zoipa m’malo mwa zabwino,+Ndipo ndimakhala wachisoni ngati wofedwa.+ Salimo 109:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Andizungulira ndi mawu achidani,+Ndipo akulimbana nane popanda chifukwa.+