Salimo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Pakuti ndasungulumwa ndipo ndasautsika.+ Salimo 86:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+
16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+